MODELING, FASHION, GRAPHIC DESIGN, DRAWING ART, GAMING, PHOTOGRAPHY, VIDEOGRAPHY, COSMETOL, AND MORE
NEW UPTOWN LODGE 24Th December MOMENTS & HIGHLIGHTS
Anthu ozisata aku BALAKA URBAN AREAS monga Majiga 2 & 1 , Andiamo , Mponda, Mangengere , Mtonya , Lime and more areas around Balaka Town afika ku new uptown lodge pa 25 december 2025 komwe akuzasangalala pokonzekela CHRISTIMAS ya chaka cha 2025.
Mwa iwo mwa achinyamata omwe afika ku malowa ndi monga SYXCTIN RODYPIANO ,ROMMIE , NESSAR, CHRISTINA, DIZE NATION and BALAKA VENDOR
Tinacheza ndi anthuwa ndipo akuti iwo akonzeka kusangalala nyengo imeneyi ya christmas komanso new year, zikuoneka kuti anthu ambiri aku abwela ku malo ano a NEW UPTOWN LODGE (ANDIAMO).
FOLLOW OUR FACEBOOK PAGE ( Balaka Entertainment Hub)
24th DECEMBER AT NEW UPTOWN LODGE
Anthu ozisata aku Majiga 2 afika ku new uptown lodge pa 24 december 2025 komwe akuzasangalala pokonzekela CHRISTIMAS ya chaka cha 2025.
Mwa iwo mwa achinyamata omwe afika ku malowa ndi monga BALAKA VENDOR, STONER KAMERA, DIZE NATION, NEEZAR AND CHRISTINA.
Tinacheza ndi anthuwa ndipo akuti iwo akonzeka kusangalala nyengo imeneyi ya christmas komanso new year, zikuoneka kuti anthu ambiri aku abwela ku malo ano a NEW UPTOWN LODGE (ANDIAMO).
FOLLOW OUR FACEBOOK PAGE ( Balaka Entertainment Hub)
WANGATA MW SANTA OF 2025 CHRISTIMAS
Modzi mwa achinyamata aku Balaka odziwika bwino pa TIKTOK dziko Muno WANGATA MW yemwe amadziwika pa TIKTOK ndi dzina loti MAI NKHUMBA. akufunila mafuno abwino anthu nonse mu nyengo ya christimas komaso new year.
iye poyankhulana ndi BALAKA ENTERTAINMENT HUB iye wati munyengo ya christmas akhala akusangalasa anthu pa TIKTOK ngati SANTA waku Balaka
FOLLOW OUR FACEBOOK PAGE # Balaka Entertainment Hub
#MODEL THEONA
THEONA NEW MODEL IN TOWN
Meet Theona, a model based in balaka and liwonde, With Two years experience in Modelling and Fashion influencing. THEONA is a model who under gone the modeling course.
Now she is Under management of director otee of FEMINDA FILMS.
Follow, like on her Social Media platforms @Theons_Model and Book THEONA through her Manager Otee.
🔥🔥🔥🌟🌟🌟🌟💯💯💯💯💖💖
#BalakaEntertainmentHub #Theona #Model
AFOTO PREMA 📸
#BALAKA_PHOTOGRAPHY_INDUSTRY📸🔥
is #Afoto_Prema a next big move in Photography?
Ambiri akusimba komaso kuyamikila za luso lamajambulidwe la Afoto Prema. yemwe akupanga magic pa editing yake ndipo iye wati ichi ndichiyambi chabe ntchito agwila pakuti izi ndizomwe anabwelela ndipo ojambula ena akumudandaula kwambiri poti walanda ma customer ndipo ena akutseka ma studio awo.
📸📸📸🔥🔥🔥🔥🎉🎉🎉🌟🌟🌟
#BalalaEntertainmenthub #Website #Photography

